Channel Avatar

Malawian Cameras @UCDhMLf1EGzLRALZ-iOYtb5w@youtube.com

56K subscribers - no pronouns :c

You're welcome to MalawianCameras YouTube Channel Here we do


Welcoem to posts!!

in the future - u will be able to do some more stuff here,,,!! like pat catgirl- i mean um yeah... for now u can only see others's posts :c

Malawian Cameras
Posted 2 days ago

#Parliament : Sameer Suleman yemwe ndi phungu wa dera la ku m'mawa cha ku mwera kwa nzinda wa Blantyre anayima kuti ayankhulepo pa zomwe mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera anayankhula mnyumbayi koma sipikala wa nyumbayi sanalole kuti atero.

Izi zinapangitsa Suleman kukhala pansi.

#mijnews #malawinews #malawi
-Alex Batison-

183 - 30

Malawian Cameras
Posted 2 weeks ago

Mwanvako Chani za Bakili Muluzi tv?

191 - 35

Malawian Cameras
Posted 3 weeks ago

Hanna Jabes( Tamia Jah ) Wafika ku Bwalo la Milandu laling'ono ku Lilongwe komwe akuyembekezeka kuyakha mlandu omwe sukudziwika pakadali pano.

Chikalata china chochokera ku bwalo la milandu,chomwe chikhala chikuzungulira mmasamba a mchezo sichinalongosole za mlandu omwe Tamia Jah akuyembekezeka kuyakha.
pano Jah akudikira oweluza milandu kuti ayambe kuuwelenga mlanduwu.

130 - 20

Malawian Cameras
Posted 3 weeks ago

7pm lero Ticheze ziwiri zitatu ndi Dennis Thanthwe Khang'a Mahata monga mwapanganoπŸ€£πŸ™

162 - 30

Malawian Cameras
Posted 1 month ago

Peter Mutharika Ayankhula usiku uno 8:30 pa zomwe zikuchitika mudziko muno.
19-01-2025. Sunday.

174 - 30

Malawian Cameras
Posted 1 month ago

https://youtu.be/yMOsmaQ2TSs?si=vQIJ5...

I am conflicted here, this is why I haven't said a word over @Eng. Mumba... I love the anger of the Minister, over I suppose the poor treatment of workers/labourers. WE SHOULD ALL BE ANGRY with many things in this country including the Corruption in the Judiciary. But his treatment of this person, is also becoz she is a woman, vulnerable. As Men, we have a tendency of speaking to women disrespectfully. That said, Eng. Mumba should never assault or attack anyone like this, male or female.
Lastly, Eng. Mumba is assault Malawians stealing BILLIONS with Nick Chakwera etc. This is why I am conflicted lol, so I won't comment on this issue. After all, I am card carrying member of MCP
Alexious Kamangila

19 - 10

Malawian Cameras
Posted 1 month ago

His Excellency President Prof Arthur Peter Mutharika wauza anthu ammadera a Che Mussa komanso Chirimba kuti akalembetse mkaundula wa mavote mmasiku oonjezera amene ayikidwa ndi bungwe loona za chisankho.

Iwo ati ngati A-malawi akufuna kuti achose Boma lovunda la MCP yankho lake ndikukalembetsa ndipo kuzavotera chipani cha DPP mchisankho chimene chikubwera mu September chaka chino.

Nzachiziwikile kuti Chakwera walephera kuyendesa Boma pamene njala, Kusowa kwa Mafuta, katangale wamanga nthenje m'dziko la Malawi.

319 - 31

Malawian Cameras
Posted 1 month ago

Mtsogoleri wa chipani cha Alliance for Democracy (AFORD) a Enock Chihana limodzi ndi wachiwiri wawo a Timothy Mtambo madzulo ano anakawaona a Joseph Mwanamvekha a chipani cha Democratic Progressive (DPP) ku police ya Lilongwe.

A Mwanamvekha ndi anthu ena anayi awamanga lero powaganizira kuti anasokoneza ndalama ku kampani ya Salima Sugar.

Malingana ndi a Chihana izi achita potengera kuti onse ndi zipani zotsutsa kotero akuyenera kukhala limodzi pa mavuto komanso pa mtendere.

(by Dickson Chivwati Gondwe-Lilongwe:12/06/25)

155 - 10

Malawian Cameras
Posted 1 month ago

ENA MWA OMWE ATAPIDWA NDAMENEWA.

145 - 30

Malawian Cameras
Posted 1 month ago

HAPPY NEW YEAR FROM MALAWIAN CAMERAS TO YOU AND YOUR FAMILY πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰πŸŽ‰

92 - 16